2 Samueli 19:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo mfumu inanyamuka, nikakhala pachipata. Ndipo anauza anthu kuti, Onani mfumu ilikukhala pachipata; anthu onse nadza pamaso pa mfumu. Koma Aisraele adathawa, munthu yense ku hema wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo mfumu inanyamuka, nikakhala pachipata. Ndipo inauza anthu kuti, Onani mfumu ilikukhala pachipata; anthu onse nadza pamaso pa mfumu. Koma Aisraele adathawa, munthu yense ku hema wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Itamva zimenezi mfumu idanyamuka, nikakhala pansi pafupi ndi chipata. Choncho anthu onse atamva kuti mfumu ili ku chipata, adabwera pamaso pa mfumuyo. Nthaŵi imeneyo nkuti Aisraele atathaŵa, aliyense kunka kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kotero mfumu inanyamuka ndipo inakhala pa mpando wake pa chipata. Pamene asilikali anawuzidwa kuti, “Mfumu yakhala pa chipata,” onse anabwera kwa iye. Nthawi imeneyi nʼkuti Aisraeli atathawira ku nyumba zawo. Onani mutuwo |