1 Samueli 8:2 - Buku Lopatulika2 Dzina la mwana wake woyamba ndiye Yowele, ndi dzina la wachiwiri ndiye Abiya; ndiwo oweruza a ku Beereseba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Dzina la mwana wake woyamba ndiye Yowele, ndi dzina la wachiwiri ndiye Abiya; ndiwo oweruza a ku Beereseba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mwana wake wachisamba anali Yowele, wachiŵiri anali Abiya. Iwoŵa ankaweruza ku Beereseba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mwana wake woyamba anali Yoweli, wachiwiri anali Abiya, ndipo ankaweruza ku Beeriseba. Onani mutuwo |