1 Samueli 8:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, pamene Samuele anakalamba, anaika ana ake aamuna akhale oweruza a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, pamene Samuele anakalamba, anaika ana ake amuna akhale oweruza a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Samuele atakalamba, adaika ana ake kuti akhale oweruza Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Samueli atakalamba anasankha ana ake kuti akhale oweruza Aisraeli. Onani mutuwo |