Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Samueli 8:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mwana wake woyamba anali Yoweli, wachiwiri anali Abiya, ndipo ankaweruza ku Beeriseba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Dzina la mwana wake woyamba ndiye Yowele, ndi dzina la wachiwiri ndiye Abiya; ndiwo oweruza a ku Beereseba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Dzina la mwana wake woyamba ndiye Yowele, ndi dzina la wachiwiri ndiye Abiya; ndiwo oweruza a ku Beereseba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mwana wake wachisamba anali Yowele, wachiŵiri anali Abiya. Iwoŵa ankaweruza ku Beereseba.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 8:2
7 Mawu Ofanana  

Kenaka Abrahamu anabwerera kumene anasiya antchito ake kuja nanyamukira nawo pamodzi kupita ku Beeriseba. Ndipo Abrahamu anakhala ku Beeriseba.


Israeli anasonkhanitsa zonse anali nazo napita ku Beeriseba kukapereka nsembe kwa Mulungu wa abambo ake Isake.


Eliya ataona zimenezi, ananyamuka nathawa kupulumutsa moyo wake. Atafika ku Beeriseba ku Yuda, anasiya mtumiki wake kumeneko,


Salumu anabereka Hilikiya, Hilikiya anabereka Azariya,


Ana a Samueli ndi awa: Mwana wake woyamba anali Yoweli, wachiwiri anali Abiya.


mwana wa Izihari, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, mwana wa Israeli;


musafunefune Beteli, musapite ku Giligala, musapite ku Beeriseba. Pakuti Giligala adzatengedwa ndithu kupita ku ukapolo, ndipo Beteli adzawonongekeratu.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa