1 Samueli 8:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ana ake sanatsanze makhalidwe ake, koma anapatukira ku chisiriro, nalandira chokometsera mlandu, naipitsa kuweruza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ana ake sanatsanze makhalidwe ake, koma anapatukira ku chisiriro, nalandira chokometsera mlandu, naipitsa kuweruza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma ana akewo sanali ndi makhalidwe abwino a bambo wao, ankapotokera ku zoipa, namatsata phindu. Ankalandira ziphuphu, namaweruza milandu mopanda chilungamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma ana akewo sanatengere makhalidwe ake abwino. Iwo ankapotokera ku zoyipa namatsata phindu mwachinyengo. Ankalandira ziphuphu ndi kumaweruza mwachinyengo. Onani mutuwo |