1 Samueli 31:6 - Buku Lopatulika6 Chomwecho adamwalira pamodzi Saulo ndi ana ake atatu, ndi wonyamula zida zake, ndi anthu ake onse, tsiku lomwe lija. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chomwecho adamwalira pamodzi Saulo ndi ana ake atatu, ndi wonyamula zida zake, ndi anthu ake onse, tsiku lomwe lija. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Motero Saulo adafa pamodzi ndi ana ake atatu, kudzanso munthu wonyamula zida zake, kuphatikizapo ankhondo ake ambiri, onsewo tsikulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Motero Sauli ndi ana ake atatu, wonyamula zida zake pamodzi ndi anthu ake onse anafera limodzi pa tsikulo. Onani mutuwo |