1 Samueli 31:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo pakuona kuti Saulo anafa, wonyamula zida zake yemwe, anagwera lupanga lake, nafera limodzi ndi iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo pakuona kuti Saulo anafa, wonyamula zida zake yemwe, anagwera lupanga lake, nafera limodzi ndi iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Wonyamula zida uja ataona kuti Saulo wafa, nayenso adadzigwetsa pa lupanga lake nafera naye limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mnyamata wonyamula zida zake uja ataona kuti Sauli wafa, nayenso anadzigwetsera pa lupanga lake nafa naye limodzi. Onani mutuwo |