1 Samueli 3:4 - Buku Lopatulika4 Pamenepo Yehova anaitana Samuele; ndipo iye anayankha kuti, Ndili pano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamenepo Yehova anaitana Samuele; ndipo iye anayankha kuti, Ndili pano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono Chauta adaitana kuti, “Samuele, Samuele!” Iye adayankha kuti, “Ŵaŵa!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yehova anayitana Samueli. Iye anayankha kuti, “Wawa.” Onani mutuwo |