1 Samueli 3:3 - Buku Lopatulika3 ndi nyali ya Mulungu isanazime, Samuele nagona mu Kachisi wa Yehova, m'mene munali likasa la Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndi nyali ya Mulungu isanazime, Samuele nagona m'Kachisi wa Yehova, m'mene munali likasa la Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Samuelenso anali gone m'Nyumba ya Chauta kumene kunali Bokosi lachipangano la Chauta. Nthaŵiyo nkuti nyale ya Mulungu isanazime. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nthawiyi nʼkuti nyale ya Mulungu isanazimitsidwe. Samueli anali gone mu Nyumba ya Yehova, kumene kunali Bokosi la Chipangano cha Mulungu. Onani mutuwo |