amene anamdzera mau a Yehova masiku a Yosiya mwana wake wa Amoni, mfumu ya Ayuda chaka chakhumi ndi chitatu cha ufumu wake.
Yoweli 1:1 - Buku Lopatulika Mau a Yehova a kwa Yowele mwana wa Petuwele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mau a Yehova a kwa Yowele mwana wa Petuwele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nawu uthenga umene Chauta adapatsa Yowele, mwana wa Petuwele: Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anayankhula ndi Yoweli mwana wa Petueli. |
amene anamdzera mau a Yehova masiku a Yosiya mwana wake wa Amoni, mfumu ya Ayuda chaka chakhumi ndi chitatu cha ufumu wake.
anadzadi mau a Yehova kwa Ezekiele wansembe, mwana wa Buzi, m'dziko la Ababiloni kumtsinje Kebara; ndi pomwepo dzanja la Yehova lidamkhalira.
Mau a Yehova amene anadza kwa Hoseya mwana wa Beeri masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu a Yuda, ndi masiku a Yerobowamu mwana wa Yowasi mfumu ya Israele.
pakuti kale lonse chinenero sichinadze ndi chifuniro cha munthu; koma anthu a Mulungu, ogwidwa ndi Mzimu Woyera, analankhula.