Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 2:16 - Buku Lopatulika

16 komatu ichi ndi chimene chinanenedwa ndi mneneri Yowele,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 komatu ichi ndi chimene chinanenedwa ndi mneneri Yowele,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Koma zimenezi ndi zomwe mneneri Yowele adalosa kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Koma izi ndi zimene ananena Mneneri Yoweli kuti:

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 2:16
5 Mawu Ofanana  

Mau a Yehova a kwa Yowele mwana wa Petuwele.


Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, sikudzakhala kuunika, zowalazo zidzada;


Pakuti awa sanaledzere monga muyesa inu; pakuti ndi ora lachitatu lokha la tsiku;


Ndipo kudzali m'masiku otsiriza, anena Mulungu, ndidzathira cha Mzimu wanga pa thupi lililonse, ndipo ana anu aamuna, ndi aakazi adzanenera, ndipo anyamata anu adzaona masomphenya, ndi akulu anu adzalota maloto;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa