Machitidwe a Atumwi 2:15 - Buku Lopatulika15 Pakuti awa sanaledzere monga muyesa inu; pakuti ndi ora lachitatu lokha la tsiku; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pakuti awa sanaledzera monga muyesa inu; pakuti ndi ora lachitatu lokha la tsiku; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Anthuŵa sadaledzere ai, monga mukuganizira inu, pakuti nthaŵi idakali 9 koloko m'maŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kunena zoona, anthu awa sanaledzere ayi, monga momwe mukuganizira, pakuti ino ndi 9 koloko mmawa! Onani mutuwo |