Hoseya 1:1 - Buku Lopatulika1 Mau a Yehova amene anadza kwa Hoseya mwana wa Beeri masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu a Yuda, ndi masiku a Yerobowamu mwana wa Yowasi mfumu ya Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mau a Yehova amene anadza kwa Hoseya mwana wa Beeri masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu a Yuda, ndi masiku a Yerobowamu mwana wa Yowasi mfumu ya Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pa nthaŵi ya ufumu wa Uziya, wa Yotamu, wa Ahazi ndi wa Hezekiya, mafumu a ku Yuda, ndiponso pamene Yerobowamu mwana wa Yowasi anali mfumu ya ku Israele, Chauta ankamupatsa uthenga Hoseya, mwana wa Beeri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Awa ndi mawu amene Yehova anayankhula kwa Hoseya mwana wa Beeri pa nthawi ya ulamuliro wa Uziya, Yotamu, Ahazi ndi Hezekiya, mafumu a ku Yuda ndiponso pa nthawi ya ulamuliro wa Yeroboamu mwana wa Yowasi mfumu ya ku Israeli. Onani mutuwo |