Danieli 12:13 - Buku Lopatulika13 Koma iwe, muka mpaka chimaliziro; pakuti udzapumula, nudzaima m'gawo lako masiku otsiriza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma iwe, muka mpaka chimaliziro; pakuti udzapumula, nudzaima m'gawo lako masiku otsiriza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 “Koma iweyo Danieli, pitiriza ndipo ulimbikire mpaka matsiriziro. Kenaka udzamwalira. Koma mʼmasiku otsiriza udzauka kuti ulandire gawo lako.” Onani mutuwo |