Yohane 4:4 - Buku Lopatulika Ndipo anayenera kupita pakati pa Samariya. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anayenera kupita pakati pa Samariya. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa ulendowo ankayenera kudzera m'dziko la Samariya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Iye anayenera kudutsa mu Samariya. |
Ndipo Iye anati kwa iwo, Kuli bwanji kuti munalikundifunafuna Ine? Simunadziwa kodi kuti kundiyenera Ine ndikhale m'zake za Atate wanga?
Ndipo tsiku la mikate yopanda chotupitsa linafika, limene inayenera kuphedwa nsembe ya Paska.