Yohane 4:3 - Buku Lopatulika3 anachokera ku Yudeya, namukanso ku Galileya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 anachokera ku Yudeya, namukanso ku Galileya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pamene Yesu adadziŵa kuti Afarisi azimva zimenezi, adachokako ku Yudeya napitanso ku Galileya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye anachoka ku Yudeya ndi kubwereranso ku Galileya. Onani mutuwo |