Luka 17:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo kunali, pakumuka ku Yerusalemu Iye analikupita pakati pa Samariya ndi Galileya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo kunali, pakumuka ku Yerusalemu Iye analikupita pakati pa Samariya ndi Galileya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pa ulendo wake wopita ku Yerusalemu, Yesu adadzera m'malire a Samariya ndi Galileya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsopano Yesu anayenda mʼmalire a pakati pa Samariya ndi Galileya pa ulendo wake wa ku Yerusalemu. Onani mutuwo |