Luka 17:10 - Buku Lopatulika10 Chotero inunso m'mene mutachita zonse anakulamulirani, nenani, Ife ndife akapolo opanda pake, tangochita zimene tayenera kuzichita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chotero inunso m'mene mutachita zonse anakulamulirani, nenani, Ife ndife akapolo opanda pake, tangochita zimene tayenera kuzichita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Choncho inunso, mutachita zonse zimene adakulamulani, muziti, ‘Ndife antchito osayenera kulandira kanthu. Tangochita zimene tinayenera kuchita.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Chimodzimodzi inunso, mukachita zonse zimene munawuzidwa, muzinena kuti, ‘Ndife antchito osayenera; tangogwira ntchito yathu basi.’ ” Onani mutuwo |