Luka 17:9 - Buku Lopatulika9 Kodi ayamika kapoloyo chifukwa anachita zolamulidwa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Kodi ayamika kapoloyo chifukwa anachita zolamulidwa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kodi ungamthokoze wantchitoyo chifukwa chakuti wachita zimene unamlamula? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kodi iye angathokoze wantchitoyo chifukwa chochita chimene anawuzidwa kuchita? Onani mutuwo |