Luka 17:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo m'mene analowa Iye m'mudzi wina, anakomana naye amuna khumi akhate, amene anaima kutali; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo m'mene analowa Iye m'mudzi wina, anakomana naye amuna khumi akhate, amene anaima kutali; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamene ankaloŵa m'mudzi wina, anthu khumi akhate adadzamchingamira. Adaima kutali, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Akulowa mʼmudzi wina, amuna khumi amene anali ndi khate anakumana naye. Iwo anayima patali Onani mutuwo |