Luka 17:13 - Buku Lopatulika13 ndipo iwo anakweza mau, nanena, Yesu, Mbuye, mutichitire chifundo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ndipo iwo anakweza mau, nanena, Yesu, Mbuye, mutichitire chifundo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 nanena mokweza mau kuti, “Yesu Ambuye, tichitireni chifundo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 ndipo anafuwula ndi mawu okweza kuti, “Yesu, Ambuye, tichitireni chifundo!” Onani mutuwo |