Luka 22:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo tsiku la mikate yopanda chotupitsa linafika, limene inayenera kuphedwa nsembe ya Paska. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo tsiku la mikate yopanda chotupitsa linafika, limene inayenera kuphedwa nsembe ya Paska. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsiku la buledi wosafufumitsa lidafika, ndiye kuti tsiku limene anthu ankapha mwanawankhosa wochitira phwando la Paska. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka linafika tsiku la buledi wopanda yisiti pamene mwana wankhosa wa Paska amaperekedwa nsembe. Onani mutuwo |