Luka 22:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo iye anavomera, nafunafuna nthawi yabwino yakumpereka Iye kwa iwo, pakalibe khamu la anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo iye anavomera, nafunafuna nthawi yabwino yakumpereka Iye kwa iwo, pakalibe khamu la anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yudasi adavomera, nayamba kufunafuna mpata woti amuperekere kwa iwo, anthu onse osadziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye anavomera, ndipo anayamba kufunafuna mpata wabwino wakuti amupereke Yesu kwa iwo pamene panalibe gulu la anthu pafupi. Onani mutuwo |