Luka 22:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Iye anatumiza Petro ndi Yohane, nati, Pitani mutikonzere ife Paska, kuti tidye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Iye anatumiza Petro ndi Yohane, nati, Pitani mutikonzere ife Paska, kuti tidye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Yesu adatuma Petro ndi Yohane naŵauza kuti, “Pitani mukatikonzere phwando la Paska kuti tikadye.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yesu anatuma Petro ndi Yohane nati, “Pitani kukatikonzera Paska kuti tikadye.” Onani mutuwo |