Luka 22:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo iwo ananena naye, Mufuna tikakonzere kuti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo iwo ananena naye, Mufuna tikakonzere kuti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma iwo adamufunsa kuti, “Kodi tikakonzere kuti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iwo anafunsa kuti, “Kodi mukufuna tikakonzere kuti?” Onani mutuwo |