Luka 22:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Iye anati kwa iwo, Onani, mutalowa m'mzinda, adzakomana ndinu munthu alikusenza mtsuko wa madzi; mumtsate ameneyo kunyumba kumene akalowako iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Iye anati kwa iwo, Onani, mutalowa m'mudzi, adzakomana ndinu munthu alikusenza mtsuko wa madzi; mumtsate ameneyo kunyumba kumene akalowako iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Yesu adati, “Mvetsani! Mukangoloŵa m'mudzimu, mukumana ndi munthu wamwamuna atasenza mtsuko wa madzi. Mukamtsatire mpaka kunyumba kumene akaloŵe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iye anayankha kuti, “Taonani, mukamalowa mu mzinda, mudzakumana ndi mwamuna atanyamula mtsuko wamadzi. Mulondoleni ku nyumba imene akalowe, Onani mutuwo |