Tsopano mwalamulidwa chitani ichi; muwatengere ana anu ndi akazi magaleta a m'dziko la Ejipito; nimubwere naye atate wanu.
Numeri 7:7 - Buku Lopatulika Anapatsa ana a Geresoni magaleta awiri ndi ng'ombe zinai, monga mwa ntchito yao; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Anapatsa ana a Geresoni magaleta awiri ndi ng'ombe zinai, monga mwa ntchito yao; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Geresoni adaŵapatsa ngolo ziŵiri ndi ng'ombe zinai potsata ntchito yao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anapereka ngolo ziwiri ndi ngʼombe zothena zinayi kwa Ageresoni monga mwantchito yawo |
Tsopano mwalamulidwa chitani ichi; muwatengere ana anu ndi akazi magaleta a m'dziko la Ejipito; nimubwere naye atate wanu.