Pemphero langa liikike ngati chofukiza pamaso panu; kukweza manja anga kuikike ngati nsembe ya madzulo.
Numeri 7:68 - Buku Lopatulika chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzaza ndi lubani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; |
Pemphero langa liikike ngati chofukiza pamaso panu; kukweza manja anga kuikike ngati nsembe ya madzulo.
ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;