Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 7:68 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

68 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

68 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

68 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

68 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzaza ndi lubani,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:68
3 Mawu Ofanana  

Pemphero langa lifike kwa Inu ngati lubani; kukweza manja kwanga kukhale ngati nsembe yamadzulo.


mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani;


mwana wangʼombe wamwamuna mmodzi, nkhosa imodzi yayimuna ndi mwana wankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, nsembe yopsereza;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa