Numeri 7:14 - Buku Lopatulika14 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide kolemera magaramu 110, kodzaza ndi lubani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwo |
Ndipo ataitsiriza, anabwera nazo ndalama zotsala kwa mfumu ndi Yehoyada, napanga nazo zipangizo za nyumba ya Yehova, zipangizo za kutumikira nazo, ndi kupereka nsembe nazo, ndi zipande, ndi zipangizo za golide ndi siliva. Ndipo anapereka kosalekeza nsembe zopsereza m'nyumba ya Yehova masiku onse a Yehoyada.