akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema;
Numeri 7:16 - Buku Lopatulika tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mbuzi yayimuna imodzi, nsembe ya machimo; |
akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema;
Ndipo wansembe atengeko mwazi wa nsembe yauchimo ndi chala chake, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wake patsinde pa guwa la nsembe yopsereza.
ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;