Levitiko 4:23 - Buku Lopatulika23 akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 pambuyo pake ena nkumudziŵitsa za tchimo lakelo, iyeyo apereke nsembe ya tonde wopanda chilema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndipo ngati wauzidwa za tchimo limene wachita, iye abwere ndi mbuzi yayimuna yopanda chilema kuti ikhale chopereka chake. Onani mutuwo |