Numeri 6:6 - Buku Lopatulika Masiku onse akudzipatulira kwa Yehova asayandikize mtembo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Masiku onse akudzipatulira kwa Yehova asayandikize mtembo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Masiku onse pamene munthuyo wadzipereka kwa Chauta, asayandikire mtembo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa nthawi yonse imene munthuyo wadzipatula yekha kwa Yehova asayandikire mtembo. |
Asatuluke m'malo opatulika, kapena kuipsa malo opatulika a Mulungu wake; popeza korona wa mafuta odzoza wa Mulungu wake ali pa iye; Ine ndine Yehova.
Kotero kuti ife sitidziwanso munthu tsopano monga mwa thupi; ndipo ngati tazindikira Khristu monga mwa thupi, koma tsopano sitimzindikiranso motero.