Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 6:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Pa nthawi yonse imene munthuyo wadzipatula yekha kwa Yehova asayandikire mtembo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Masiku onse akudzipatulira kwa Yehova asayandikize mtembo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Masiku onse akudzipatulira kwa Yehova asayandikize mtembo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 “Masiku onse pamene munthuyo wadzipereka kwa Chauta, asayandikire mtembo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 6:6
10 Mawu Ofanana  

“ ‘Musadzichekecheke pathupi panu chifukwa cha munthu wakufa kapena kudzitema mphini pa thupi lanu. Ine ndine Yehova.


Asalowe mʼnyumba mmene muli munthu wakufa ngakhale womwalirayo ndi amayi ake kapena abambo ake.


Asadzidetse potulukira kunja kwa malo opatulika popeza mafuta womupatula kukhala wansembe ali pamutu pake. Ine ndine Yehova.


Choncho, kuyambira tsopano mpaka mʼtsogolo ife sitiganizirapo za munthu aliyense monga mwanzeru za umunthu, ngakhale kuti poyamba tinkaganiza za Khristu mʼnjira imeneyi, koma tsopano sititeronso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa