Ndipo ana onse a Israele anadandaulira Mose ndi Aroni; ndi khamu lonse linanena nao, Mwenzi tikadafa m'dziko la Ejipito; kapena mwenzi tikadafa m'chipululu muno!
Numeri 32:8 - Buku Lopatulika Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza achoke ku Kadesi-Baranea kukaona dziko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza achoke ku Kadesi-Baranea kukaona dziko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Makolo anu adachita zotero, pamene ndidaŵatuma kuchokera ku Kadesi-Baranea, kuti akaone dziko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Izi ndi zimene makolo anu anachita pamene ndinawatuma kuchokera ku Kadesi kukaona dzikolo. |
Ndipo ana onse a Israele anadandaulira Mose ndi Aroni; ndi khamu lonse linanena nao, Mwenzi tikadafa m'dziko la Ejipito; kapena mwenzi tikadafa m'chipululu muno!
ndi malire anu adzapinda kuchokera kumwera kunka pokwera Akarabimu, ndi kupitirira ku Zini; ndi kutuluka kwake adzachokera kumwera ku Kadesi-Baranea, nadzatuluka kunka ku Hazara-Adara, ndi kupita kunka ku Azimoni;
Ulendo wake wochokera ku Horebu wofikira ku Kadesi-Baranea, wodzera njira ya phiri la Seiri, ndiwo wa masiku khumi ndi limodzi.