Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 32:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Izi ndi zimene makolo anu anachita pamene ndinawatuma kuchokera ku Kadesi kukaona dzikolo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza achoke ku Kadesi-Baranea kukaona dziko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza achoke ku Kadesi-Baranea kukaona dziko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Makolo anu adachita zotero, pamene ndidaŵatuma kuchokera ku Kadesi-Baranea, kuti akaone dziko.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:8
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Aisraeli onse anayankhula motsutsana ndi Mose ndi Aaroni. Gulu lonse linanena kwa iwo kuti, “Kunali bwino tikanafera ku Igupto kapena mʼchipululu muno!


Malirewo adzapita kummwera ndipo adzakwera phiri la Akirabimu mpaka ku Zini. Mathero ake adzakhala kummwera kwa Kadesi-Baranea. Ndipo adzapitenso ku Hazari Adari mpaka kukafika ku Azimoni,


(Kuyenda kuchokera ku Horebu kukafika ku Kadesi Barinea kudzera njira ya ku Phiri la Seiri ndi ulendo wa masiku khumi ndi limodzi).


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa