Numeri 32:10 - Buku Lopatulika Ndipo Yehova anapsa mtima tsiku lija, nalumbira Iye, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova anapsa mtima tsiku lija, nalumbira Iye, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono pa tsiku limenelo Chauta adapsa mtima, ndipo adalumbira kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anakwiya tsiku limenelo ndipo analumbira kuti, |
Ndipo ndinawakwezeranso dzanja langa m'chipululu, kusawalowetsa m'dzikolo ndidawapatsa, moyenda mkaka ndi uchi, ndilo lokometsetsa mwa maiko onse;
Ndipo Yehova anati kwa Mose, Anthu awa adzaleka liti kundinyoza? Ndipo adzayamba liti kundikhulupirira, chinkana zizindikiro zonse ndinazichita pakati pao?
sadzaona dzikoli ndidalumbirira makolo ao, ngakhale mmodzi wa iwo akundinyoza Ine, sadzaliona;
mitembo yanu idzagwa m'chipululu muno; ndi owerengedwa anu onse, monga mwa kuwerenga kwani konse, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, akudandaula pa Ine;