Numeri 14:21 - Buku Lopatulika21 koma ndithu, pali Ine, dziko lonse lapansi lidzadzazidwa ndi ulemerero wa Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 koma ndithu, pali Ine, dziko lonse lapansi lidzadzazidwa ndi ulemerero wa Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma ndikulumbira kuti pali Ine ndemwe ndiponso malinga nkuti dziko lonse lapansi ndi lodzaza ndi ulemerero wa Chauta, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Komabe, ndikunenetsa kuti pali Ine, ndiponso pamene dziko lapansi ladzaza ndi ulemerero wa Yehova, Onani mutuwo |
Chifukwa chake, pali moyo wanga, ati Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele, Zedi Mowabu adzakhala ngati Sodomu, ndi ana a Amoni ngati Gomora, pochuluka khwisa ndi maenje a mchere, ndi bwinja losatha; otsala a anthu anga adzalanda zao, ndi otsala a mtundu wa anthu anga adzawalandira akhale cholowa chao.