Numeri 14:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Yehova anati, Ndakhululukira monga mwa mau ako: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Yehova anati, Ndakhululukira monga mwa mau ako: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Chauta adati, “Ndaŵakhululukira chifukwa cha mau ako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Yehova anayankha kuti, “Ndawakhululukira monga wapemphera. Onani mutuwo |