Ndipo Aroni anadzitengera Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Nasoni, akhale mkazi wake; ndipo anambalira Nadabu ndi Abihu, Eleazara ndi Itamara.
Numeri 26:60 - Buku Lopatulika Ndipo Nadabu ndi Abihu, Eleazara ndi Itamara anabadwira Aroni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Nadabu ndi Abihu, Eleazara ndi Itamara anabadwira Aroni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Aroni adabala Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Aaroni anali abambo a Nadabu, Abihu, Eliezara ndi Itamara. |
Ndipo Aroni anadzitengera Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wake wa Nasoni, akhale mkazi wake; ndipo anambalira Nadabu ndi Abihu, Eleazara ndi Itamara.
Ndipo maina ao a ana aamuna a Aroni ndi awa: Woyamba Nadabu, ndi Abihu, Eleazara, ndi Itamara.
Ndipo asunge zipangizo zonse za chihema chokomanako, ndi udikiro wa ana a Israele, kuichita ntchito ya Kachisi.