Numeri 26:61 - Buku Lopatulika61 Koma Nadabu ndi Abihu adafa, muja anabwera nao moto wachilendo pamaso pa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201461 Koma Nadabu ndi Abihu adafa, muja anabwera nao moto wachilendo pamaso pa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa61 Koma Nadabu ndi Abihu adafa chifukwa adaapereka moto wosaloledwa pamaso pa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero61 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamene anapereka nsembe pamaso pa Yehova ndi moto wachilendo). Onani mutuwo |