Numeri 3:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo asunge zipangizo zonse za chihema chokomanako, ndi udikiro wa ana a Israele, kuichita ntchito ya Kachisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo asunge zipangizo zonse za chihema chokomanako, ndi udikiro wa ana a Israele, kuichita ntchito ya Kachisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Aziyang'anira zipangizo zonse za m'chihema chamsonkhano, ndipo azigwirira Aisraele ntchito potumikira m'Chihema cha Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Azisamalira zipangizo zonse za mu tenti ya msonkhano, ndipo azigwirira ntchito Aisraeli potumikira mu tenti. Onani mutuwo |