Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.
Numeri 26:16 - Buku Lopatulika Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ozini anali kholo la banja la Aozini. Eri anali kholo la banja la Aeri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera mwa Ozini, fuko la Aozini; kuchokera mwa Eri, fuko la Aeri; |
Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.
Ana aamuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Suni;