Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 46:16 - Buku Lopatulika

16 Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndi ana amuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Ana a Gadi anali aŵa: Zifiyoni, Hagi, Suni, Eziboni, Eri, Arodi ndi Areli.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Ana aamuna a Gadi ndi awa: Zifioni, Hagi, Suni, Eziboni, Eri, Arodi ndi Areli.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:16
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Leya anati, Wamwai ine! Ndipo anamutcha dzina lake Gadi.


ndipo ana aamuna a Zilipa mdzakazi wake wa Leya: ndiwo Gadi ndi Asere: amenewo ndi ana aamuna a Yakobo amene anabala iye mu Padanaramu.


Amenewo ndi ana aamuna a Leya, amene anambalira Yakobo ku Padanaramu, pamodzi ndi mwana wamkazi wake Dina; ana aamuna ndi aakazi onse ndiwo anthu makumi atatu kudza atatu.


Ndi Gadi, achifwamba adzampsinja iye; koma iye adzapsinja pa chitendeni chao.


Dani, Yosefe, ndi Benjamini, Nafutali, Gadi, ndi Asere.


Wa Benjamini, Abidani mwana wa Gideoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa