Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 46:17 - Buku Lopatulika

17 Ndi ana aamuna a Asere: Imina, ndi Isiva, ndi Isivi, ndi Beriya, ndi Sera mlongo wao; ndi ana a Beriya: Hebere, ndi Malikiele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndi ana amuna a Asere: Imina, ndi Isiva, ndi Isivi, ndi Beriya, ndi Sera mlongo wao; ndi ana a Beriya: Hebere, ndi Malikiele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Ana a Asere anali aŵa: Imina, Isiva, Isivi, Beriya ndi mlongo wao Sera. Ana a Beriya anali aŵa: Hebere ndi Malikiele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ana aamuna a Aseri ndi awa: Imuna, Isiva, Isivi, Beriya ndi Sera mlongo wawo. Ana aamuna a Beriya ndi awa: Heberi ndi Malikieli.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 46:17
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Leya anati, Ndakondwa ine! Chifukwa kuti ana aakazi adzanditcha ine wokondwa: ndipo anamutcha dzina lake Asere.


ndipo ana aamuna a Zilipa mdzakazi wake wa Leya: ndiwo Gadi ndi Asere: amenewo ndi ana aamuna a Yakobo amene anabala iye mu Padanaramu.


Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.


Ndi Asere, chakudya chake ndicho mafuta, ndipo adzapereka zolongosoka zachifumu.


Dani, Yosefe, ndi Benjamini, Nafutali, Gadi, ndi Asere.


Wa Asere, Pagiyele mwana wa Okarani.


Ndi za Asere anati, Asere adalitsidwe mwa anawo; akhale wovomerezeka mwa abale ake, aviike phazi lake m'mafuta.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa