Ndi ana aamuna a Simeoni: Yemuwele ndi Yamini, ndi Ohadi, ndi Yakini, ndi Zohari, ndi Shaulo, mwana wamwamuna wa mkazi wa ku Kanani.
Numeri 26:13 - Buku Lopatulika Zera, ndiye kholo la banja la Azera; Shaulo, ndiye kholo la banja la Ashaulo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Zera, ndiye kholo la banja la Azera; Shaulo, ndiye kholo la banja la Ashaulo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Zera anali kholo la banja la Azera. Shaulo anali kholo la banja la Ashaulo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera mwa Zera, mbumba ya Zera; kuchokera mwa Sauli, fuko la Asauli. |
Ndi ana aamuna a Simeoni: Yemuwele ndi Yamini, ndi Ohadi, ndi Yakini, ndi Zohari, ndi Shaulo, mwana wamwamuna wa mkazi wa ku Kanani.
Wachisanu ndi chitatu wa mwezi wachisanu ndi chitatu ndiye Sibekai Muhusa wa Azera; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Wakhumi wa mwezi wakhumi ndiye Maharai Mnetofa wa Azera; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Ana aamuna a Simeoni monga mwa mabanja ao ndiwo: Nemuwele, ndiye kholo la banja la Anemuwele; Yamini, ndiye kholo la banja la Ayamini; Yakini, ndiye kholo la banja la Ayakini;
nayandikizitsa zibale za Yuda, nagwira chibale cha Azera; nayandikizitsa chibale cha Azera, mmodzimmodzi, nagwidwa Zabidi;