Numeri 26:1 - Buku Lopatulika Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Utatha mliriwo, Chauta adauza Mose ndi Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Utatha mliri Yehova anati kwa Mose ndi Eliezara mwana wa Aaroni, |
popeza akusautsani ndi manyengo ao amene anakunyengani nao; m'chija cha Peori, ndi cha Kozibi, mwana wamkazi wa kalonga wa ku Midiyani, mlongo wao, amene adamupha tsiku la mliri, m'chija cha Peori.