Numeri 1:19 - Buku Lopatulika19 Monga Yehova analamula Mose, momwemo anawawerenga m'chipululu cha Sinai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Monga Yehova anauza Mose, momwemo anawawerenga m'chipululu cha Sinai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 monga momwe Chauta adaalamulira Mose. Umu ndi m'mene adaŵerengera anthuwo m'chipululu cha Sinai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 monga momwe Yehova analamulira Mose. Motero iyeyo anawawerenga mʼchipululu cha Sinai: Onani mutuwo |