Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:19 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 monga momwe Yehova analamulira Mose. Motero iyeyo anawawerenga mʼchipululu cha Sinai:

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

19 Monga Yehova analamula Mose, momwemo anawawerenga m'chipululu cha Sinai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Monga Yehova anauza Mose, momwemo anawawerenga m'chipululu cha Sinai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 monga momwe Chauta adaalamulira Mose. Umu ndi m'mene adaŵerengera anthuwo m'chipululu cha Sinai.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:19
10 Mawu Ofanana  

Solomoni anawerenga alendo onse amene anali mu Israeli, potsatira chiwerengero chimene abambo ake Davide anachita ndipo panapezeka kuti analipo anthu 153,600.


Mose anachita zonse monga Yehova anamulamulira.


Iwo amasamba nthawi zonse akamalowa mu tenti ya msonkhano kapena kuyandikira guwa lansembe monga Yehova analamulira Mose.


“Werengani Aisraeli onse mʼmafuko awo ndi mʼmabanja awo, lemba dzina la munthu wamwamuna aliyense, mmodzimmodzi.


Choncho Aisraeli anachita monga Yehova analamulira Mose.


Choncho Aisraeli anachita zonse zomwe Yehova analamulira Mose. Umo ndi momwe amamangira misasa yawo pamene panali mbendera zawo, ndipo ankasamuka monga mwa mafuko a makolo awo.


Awa ndi amene anawerengedwa ndi Mose ndi Eliezara wansembe pamene ankawerenga Aisraeli pa zigwa za ku Mowabu mʼmbali mwa Yorodani ku Yeriko.


Mose anapereka ndalama zowombolera zija kwa Aaroni ndi ana ake aamuna monga mwa mawu amene Yehova analamulira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa