Ndipo Yehova anamvera mau a Israele, napereka Akanani; ndipo anawaononga konse ndi mizinda yao yomwe; natcha dzina lake la malowo Horoma.
Numeri 22:2 - Buku Lopatulika Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israele anachitira Aamori. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israele anachitira Aamori. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Balaki mwana wa Zipora adaona zonse zimene Aisraele adachita Aamori. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono Balaki mwana wa Zipori anaona zonse zimene Aisraeli anachitira Aamori, |
Ndipo Yehova anamvera mau a Israele, napereka Akanani; ndipo anawaononga konse ndi mizinda yao yomwe; natcha dzina lake la malowo Horoma.
Pamenepo Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, anauka naponyana ndi Israele; natuma naitana Balamu mwana wa Beori atemberere inu;
Ndipo tsopano kodi inu ndinu wabwino woposa Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu; anatengana konse ndi Israele iyeyu kodi, kapena kuchita nao nkhondo konse kodi?